Numeri 18:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Chamoyo chilichonse chotsegula mimba ya mayi ake,+ chimene chiziperekedwa kwa Yehova, kaya ndi munthu kapena nyama, chizikhala chako. Komabe, uzionetsetsa kuti ukuwombola mwana woyamba kubadwa wa munthu.+ Uziwombolanso+ mwana woyamba kubadwa wa nyama yodetsedwa. Deuteronomo 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Nsembe zanu zopsereza+ ndi nsembe zina, zopereka zanu za chakhumi,*+ chopereka chochokera m’manja mwanu,+ nsembe zanu za lonjezo,+ nsembe zanu zaufulu,+ ana oyamba kubadwa a ng’ombe ndi a nkhosa zanu,+ zonsezi muzidzazibweretsa kumalo amenewo.
15 “Chamoyo chilichonse chotsegula mimba ya mayi ake,+ chimene chiziperekedwa kwa Yehova, kaya ndi munthu kapena nyama, chizikhala chako. Komabe, uzionetsetsa kuti ukuwombola mwana woyamba kubadwa wa munthu.+ Uziwombolanso+ mwana woyamba kubadwa wa nyama yodetsedwa.
6 Nsembe zanu zopsereza+ ndi nsembe zina, zopereka zanu za chakhumi,*+ chopereka chochokera m’manja mwanu,+ nsembe zanu za lonjezo,+ nsembe zanu zaufulu,+ ana oyamba kubadwa a ng’ombe ndi a nkhosa zanu,+ zonsezi muzidzazibweretsa kumalo amenewo.