Numeri 18:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Pamphatso zonse zosiyanasiyana zoperekedwa kwa inu, inunso muziperekapo chopereka kwa Yehova. Muzipereka gawo lake labwino koposa,+ monga chinthu chopatulika chimene iwo apereka.’
29 Pamphatso zonse zosiyanasiyana zoperekedwa kwa inu, inunso muziperekapo chopereka kwa Yehova. Muzipereka gawo lake labwino koposa,+ monga chinthu chopatulika chimene iwo apereka.’