Yoswa 10:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pamenepo Adoni-zedeki mfumu ya Yerusalemu+ anatumiza uthenga kwa Hohamu mfumu ya ku Heburoni,+ kwa Piramu mfumu ya ku Yarimuti,+ kwa Yafiya mfumu ya ku Lakisi+ ndi kwa Debiri mfumu ya ku Egiloni.+ Anatumiza uthenga wakuti: Yoswa 15:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Lakisi,+ Bozikati,+ Egiloni,+ Yesaya 37:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Rabisake+ anali atamva kuti mfumu ya Asuri yachoka ku Lakisi,+ choncho anabwerera kwa mfumuyo n’kukaipeza ikumenyana ndi Libina.+
3 Pamenepo Adoni-zedeki mfumu ya Yerusalemu+ anatumiza uthenga kwa Hohamu mfumu ya ku Heburoni,+ kwa Piramu mfumu ya ku Yarimuti,+ kwa Yafiya mfumu ya ku Lakisi+ ndi kwa Debiri mfumu ya ku Egiloni.+ Anatumiza uthenga wakuti:
8 Rabisake+ anali atamva kuti mfumu ya Asuri yachoka ku Lakisi,+ choncho anabwerera kwa mfumuyo n’kukaipeza ikumenyana ndi Libina.+