Ekisodo 19:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndipo Yehova anauza Mose kuti: “Pita kwa anthu, uwayeretse lero ndi mawa, ndipo achape zovala zawo.+ 2 Mbiri 29:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno anawauza kuti: “Tamverani Alevi inu. Dziyeretseni+ ndipo muyeretsenso nyumba ya Yehova Mulungu wa makolo anu. Mutulutse chinthu chodetsedwa m’malo oyera.+
10 Ndipo Yehova anauza Mose kuti: “Pita kwa anthu, uwayeretse lero ndi mawa, ndipo achape zovala zawo.+
5 Ndiyeno anawauza kuti: “Tamverani Alevi inu. Dziyeretseni+ ndipo muyeretsenso nyumba ya Yehova Mulungu wa makolo anu. Mutulutse chinthu chodetsedwa m’malo oyera.+