Nehemiya 3:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Anetini+ anali kukhala ku Ofeli.+ Iwonso anakonza mpandawo mpaka kukafika ku Chipata cha Kumadzi,+ kum’mawa. Iwo anakonzanso nsanja yotundumukira kunja kwa mpanda. Nehemiya 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno anthu onse anasonkhana pamodzi mogwirizana+ m’bwalo lalikulu+ limene linali pafupi ndi Chipata cha Kumadzi.+ Pamenepo anthuwo anauza Ezara+ wokopera Malemba kuti abweretse buku+ la chilamulo cha Mose+ limene Yehova analamula Aisiraeli kuti azilitsatira.+
26 Anetini+ anali kukhala ku Ofeli.+ Iwonso anakonza mpandawo mpaka kukafika ku Chipata cha Kumadzi,+ kum’mawa. Iwo anakonzanso nsanja yotundumukira kunja kwa mpanda.
8 Ndiyeno anthu onse anasonkhana pamodzi mogwirizana+ m’bwalo lalikulu+ limene linali pafupi ndi Chipata cha Kumadzi.+ Pamenepo anthuwo anauza Ezara+ wokopera Malemba kuti abweretse buku+ la chilamulo cha Mose+ limene Yehova analamula Aisiraeli kuti azilitsatira.+