Salimo 81:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 81 Anthu inu, fuulani mosangalala kwa Mulungu amene ndi mphamvu yathu,+Fuulirani Mulungu wa Yakobo mosangalala chifukwa wapambana.+ Salimo 100:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 100 Fuulirani Yehova mosangalala inu nonse anthu a padziko lapansi chifukwa wapambana.+ Yesaya 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Fuula mwachisangalalo iwe mkazi wokhala mu Ziyoni, pakuti Woyera wa Isiraeli ndi wamkulu pakati pako.”+
81 Anthu inu, fuulani mosangalala kwa Mulungu amene ndi mphamvu yathu,+Fuulirani Mulungu wa Yakobo mosangalala chifukwa wapambana.+
6 “Fuula mwachisangalalo iwe mkazi wokhala mu Ziyoni, pakuti Woyera wa Isiraeli ndi wamkulu pakati pako.”+