1 Mbiri 9:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pa alonda a pazipatawo panali amuna anayi amphamvu amene anali pa udindo wawo chifukwa cha kukhulupirika kwawo. Amunawo anali Alevi, ndipo anali kuyang’anira zipinda zodyera+ ndi chuma+ cha m’nyumba ya Mulungu woona. 2 Mbiri 31:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pamenepo Hezekiya anawauza kuti akonze zipinda zodyera+ m’nyumba ya Yehova, ndipo iwo anakonzadi.
26 Pa alonda a pazipatawo panali amuna anayi amphamvu amene anali pa udindo wawo chifukwa cha kukhulupirika kwawo. Amunawo anali Alevi, ndipo anali kuyang’anira zipinda zodyera+ ndi chuma+ cha m’nyumba ya Mulungu woona.