Numeri 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Itanitsa fuko la Levi+ ndipo uwapereke kwa wansembe Aroni kuti azimutumikira.+ 1 Mbiri 23:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ntchito yawo inali yotumidwa ndi ana a Aroni+ pa utumiki wa panyumba ya Yehova m’mabwalo a nyumbayo,+ m’zipinda zodyeramo,+ pa ntchito yoyeretsa chinthu chilichonse chopatulika,+ ndiponso pa ntchito yotumikira panyumba ya Mulungu woona.
28 Ntchito yawo inali yotumidwa ndi ana a Aroni+ pa utumiki wa panyumba ya Yehova m’mabwalo a nyumbayo,+ m’zipinda zodyeramo,+ pa ntchito yoyeretsa chinthu chilichonse chopatulika,+ ndiponso pa ntchito yotumikira panyumba ya Mulungu woona.