Ezara 9:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsopano pambuyo pa zonse zimene zatigwera chifukwa cha zochita zathu zoipa+ ndi machimo athu ochuluka, ngakhale kuti inuyo Mulungu wathu simunatilange monga mmene tinafunika kulangidwira+ ndipo mwalola kuti anthu onsewa apulumuke,+
13 Tsopano pambuyo pa zonse zimene zatigwera chifukwa cha zochita zathu zoipa+ ndi machimo athu ochuluka, ngakhale kuti inuyo Mulungu wathu simunatilange monga mmene tinafunika kulangidwira+ ndipo mwalola kuti anthu onsewa apulumuke,+