Danieli 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Nthawi yomweyo iwo anauza mfumuyo kuti: “Danieli,+ mmodzi wa anthu amene anatengedwa ukapolo ku Yuda,+ sanakumvereni mfumu komanso sanamvere lamulo limene munasainira ndipo akupemphera katatu pa tsiku.”+
13 Nthawi yomweyo iwo anauza mfumuyo kuti: “Danieli,+ mmodzi wa anthu amene anatengedwa ukapolo ku Yuda,+ sanakumvereni mfumu komanso sanamvere lamulo limene munasainira ndipo akupemphera katatu pa tsiku.”+