Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Esitere 5:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Pamapeto pake, Hamani anatuluka tsiku limenelo ali wokondwa+ komanso akusangalala kwambiri mumtima mwake. Koma atangoona Moredekai pachipata cha mfumu+ komanso kuti sanaimirire+ ndi kunthunthumira chifukwa cha iye,+ nthawi yomweyo Hamani anamukwiyira kwambiri+ Moredekai.

  • Miyambo 12:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Munthu amene amasonyeza mkwiyo wake tsiku lomwelo ndi wopusa,+ koma wochenjera akachitiridwa chipongwe, amangozinyalanyaza.+

  • Miyambo 27:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Mwala umalemera ndiponso mchenga umalemera ukaunyamula,+ koma kusautsa kwa munthu wopusa kumalemera kwambiri kuposa zonsezi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena