Genesis 32:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mukamuuzenso kuti, ‘Ndiponso kapolo wanu Yakobo ali m’mbuyo mwathumu.’”+ Popeza mumtima mwake anati: “Mwina ndingamusangalatse potsogoza mphatsoyi,+ ndipo pambuyo pake ndingathe kuonana naye pamasom’pamaso, kuti mwina angandilandire bwino.”+ Miyambo 17:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mphatso ndiyo mwala wamtengo wapatali m’maso mwa mwiniwake wolemekezeka.+ Kulikonse kumene amapita zinthu zimamuyendera bwino.+
20 Mukamuuzenso kuti, ‘Ndiponso kapolo wanu Yakobo ali m’mbuyo mwathumu.’”+ Popeza mumtima mwake anati: “Mwina ndingamusangalatse potsogoza mphatsoyi,+ ndipo pambuyo pake ndingathe kuonana naye pamasom’pamaso, kuti mwina angandilandire bwino.”+
8 Mphatso ndiyo mwala wamtengo wapatali m’maso mwa mwiniwake wolemekezeka.+ Kulikonse kumene amapita zinthu zimamuyendera bwino.+