Miyambo 3:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Usalephere kuchitira zabwino anthu amene akufunikira zabwinozo,+ pamene dzanja lako lingathe kuchita zimenezo.+ Mlaliki 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mumzindawo munali munthu wina wosauka koma wanzeru, amene anapulumutsa mzindawo chifukwa cha nzeru zake.+ Koma kenako palibe amene anakumbukira munthu wosaukayo.+
27 Usalephere kuchitira zabwino anthu amene akufunikira zabwinozo,+ pamene dzanja lako lingathe kuchita zimenezo.+
15 Mumzindawo munali munthu wina wosauka koma wanzeru, amene anapulumutsa mzindawo chifukwa cha nzeru zake.+ Koma kenako palibe amene anakumbukira munthu wosaukayo.+