Genesis 41:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Ndiponso, anamukweza pagaleta* lachiwiri laulemu limene anali nalo,+ ndipo anthu anali kufuula patsogolo pake kuti, “A·vrékh!”* posonyeza kuti ndi wamkulu m’dziko lonse la Iguputo. 2 Samueli 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno pambuyo pa zinthu zimenezi, Abisalomu anadzipangira galeta lokokedwa ndi mahatchi, ndipo amuna 50 anali kuthamanga patsogolo pake.+
43 Ndiponso, anamukweza pagaleta* lachiwiri laulemu limene anali nalo,+ ndipo anthu anali kufuula patsogolo pake kuti, “A·vrékh!”* posonyeza kuti ndi wamkulu m’dziko lonse la Iguputo.
15 Ndiyeno pambuyo pa zinthu zimenezi, Abisalomu anadzipangira galeta lokokedwa ndi mahatchi, ndipo amuna 50 anali kuthamanga patsogolo pake.+