1 Akorinto 11:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 ndiponso mwamuna sanalengedwere mkazi, koma mkazi analengedwera mwamuna.+ Aefeso 5:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndipotu, monga mmene mpingo umagonjerera Khristu, akazinso agonjere amuna awo m’chilichonse.+