Esitere 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Hamani atalowa, mfumu inam’funsa kuti: “Kodi munthu amene mfumu yafuna kum’patsa ulemu tim’chitire chiyani?”+ Atamva zimenezi, Hamani ananena mumtima mwake kuti: “Kodi winanso ndani amene mfumu ingafune kum’patsa ulemu kuposa ine?”+
6 Hamani atalowa, mfumu inam’funsa kuti: “Kodi munthu amene mfumu yafuna kum’patsa ulemu tim’chitire chiyani?”+ Atamva zimenezi, Hamani ananena mumtima mwake kuti: “Kodi winanso ndani amene mfumu ingafune kum’patsa ulemu kuposa ine?”+