Miyambo 25:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Woipa akachotsedwa pamaso pa mfumu,+ mpando wake wachifumu udzakhazikitsidwa ndi chilungamo.+ Yesaya 13:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Nthaka ndidzaibwezera zoipa zake,+ ndipo anthu oipa ndidzawabwezera zolakwa zawo. Kunyada kwa anthu odzikuza ndidzakuthetsa, ndipo ndidzatsitsa olamulira ankhanza ndi odzikweza.+
11 Nthaka ndidzaibwezera zoipa zake,+ ndipo anthu oipa ndidzawabwezera zolakwa zawo. Kunyada kwa anthu odzikuza ndidzakuthetsa, ndipo ndidzatsitsa olamulira ankhanza ndi odzikweza.+