Esitere 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsiku limenelo, Mfumu Ahasiwero inapereka kwa mfumukazi Esitere nyumba ya Hamani,+ amene anali kuchitira nkhanza Ayuda.+ Ndipo Moredekai anabwera pamaso pa mfumu chifukwa Esitere anali atauza mfumu ubale umene unalipo pakati pawo.+ Miyambo 13:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Munthu wabwino adzasiyira cholowa zidzukulu zake, ndipo chuma cha wochimwa chimasungidwa kuti chidzakhale cha munthu wolungama.+
8 Tsiku limenelo, Mfumu Ahasiwero inapereka kwa mfumukazi Esitere nyumba ya Hamani,+ amene anali kuchitira nkhanza Ayuda.+ Ndipo Moredekai anabwera pamaso pa mfumu chifukwa Esitere anali atauza mfumu ubale umene unalipo pakati pawo.+
22 Munthu wabwino adzasiyira cholowa zidzukulu zake, ndipo chuma cha wochimwa chimasungidwa kuti chidzakhale cha munthu wolungama.+