Salimo 71:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Anthu otsutsana nane achite manyazi, iwo awonongedwe.+Amene akufunafuna kundigwetsera tsoka adziphimbe ndi chitonzo ndiponso manyazi.+ Salimo 71:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ngakhalenso lilime langa lidzalankhula chapansipansi za chilungamo chanu tsiku lonse,+Pakuti ofunafuna kundigwetsera tsoka achita manyazi ndipo athedwa nzeru.+
13 Anthu otsutsana nane achite manyazi, iwo awonongedwe.+Amene akufunafuna kundigwetsera tsoka adziphimbe ndi chitonzo ndiponso manyazi.+
24 Ngakhalenso lilime langa lidzalankhula chapansipansi za chilungamo chanu tsiku lonse,+Pakuti ofunafuna kundigwetsera tsoka achita manyazi ndipo athedwa nzeru.+