Esitere 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 M’masiku a Ahasiwero,*+ amene anali kulamulira zigawo 127 monga mfumu, kuchokera ku Indiya mpaka ku Itiyopiya,+ Danieli 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno Dariyo anaona kuti ndi bwino kuti aike masatarapi* 120 oyang’anira zigawo zonse za ufumu wake.+
1 M’masiku a Ahasiwero,*+ amene anali kulamulira zigawo 127 monga mfumu, kuchokera ku Indiya mpaka ku Itiyopiya,+
6 Ndiyeno Dariyo anaona kuti ndi bwino kuti aike masatarapi* 120 oyang’anira zigawo zonse za ufumu wake.+