Deuteronomo 21:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Pakakhala munthu amene wachita tchimo loyenera chiweruzo choti aphedwe, ndiyeno munthuyo waphedwa,+ ndipo wam’pachika pamtengo,+ Esitere 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Choncho nkhani imeneyi anaifufuza ndipo pamapeto pake zonse zinadziwika, ndipo onse awiri, Bigitana ndi Teresi anapachikidwa+ pamtengo.+ Kenako zimenezi zinalembedwa pamaso pa mfumu m’buku la zochitika+ za m’masiku amenewo. Esitere 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho anapachika Hamani pamtengo+ umene anakonzera Moredekai,+ ndipo mkwiyo wa mfumu unatha. Agalatiya 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Khristu anatigula+ ndi kutimasula+ ku temberero la Chilamulo ndipo iyeyo anakhala temberero+ m’malo mwa ife, chifukwa Malemba amati: “Ndi wotembereredwa aliyense wopachikidwa pamtengo.”+
22 “Pakakhala munthu amene wachita tchimo loyenera chiweruzo choti aphedwe, ndiyeno munthuyo waphedwa,+ ndipo wam’pachika pamtengo,+
23 Choncho nkhani imeneyi anaifufuza ndipo pamapeto pake zonse zinadziwika, ndipo onse awiri, Bigitana ndi Teresi anapachikidwa+ pamtengo.+ Kenako zimenezi zinalembedwa pamaso pa mfumu m’buku la zochitika+ za m’masiku amenewo.
13 Khristu anatigula+ ndi kutimasula+ ku temberero la Chilamulo ndipo iyeyo anakhala temberero+ m’malo mwa ife, chifukwa Malemba amati: “Ndi wotembereredwa aliyense wopachikidwa pamtengo.”+