Salimo 124:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Yehova akanapanda kukhala kumbali yathu,+Pamene anthu anatiukira,+ Salimo 124:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yehova atamandike, chifukwa sanatipereke kwa iwo+Kuti atikhadzule ngati nyama.+
2 “Yehova akanapanda kukhala kumbali yathu,+Pamene anthu anatiukira,+ Salimo 124:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yehova atamandike, chifukwa sanatipereke kwa iwo+Kuti atikhadzule ngati nyama.+