Esitere 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndipo m’zigawo zonse,+ kulikonse kumene mawu a mfumu ndi lamulo lake zinafika, Ayuda anali ndi chisoni kwambiri+ ndipo anali kusala kudya,+ kubuma ndi kulira mofuula. Ambiri anayala ziguduli+ ndi kuwazapo phulusa+ kuti agonepo.
3 Ndipo m’zigawo zonse,+ kulikonse kumene mawu a mfumu ndi lamulo lake zinafika, Ayuda anali ndi chisoni kwambiri+ ndipo anali kusala kudya,+ kubuma ndi kulira mofuula. Ambiri anayala ziguduli+ ndi kuwazapo phulusa+ kuti agonepo.