Genesis 41:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Zimene Yosefe ananena zinakomera Farao ndi antchito ake onse.+ Esitere 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mtsikana amene mtima wanu mfumu udzakondwere naye adzakhala mfumukazi m’malo mwa Vasiti.”+ Mawu amenewa anasangalatsa mfumu, ndipo inachitadi zomwezo.
4 Mtsikana amene mtima wanu mfumu udzakondwere naye adzakhala mfumukazi m’malo mwa Vasiti.”+ Mawu amenewa anasangalatsa mfumu, ndipo inachitadi zomwezo.