Ezara 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Koresi mfumu ya Perisiya wanena kuti,+ ‘Yehova Mulungu wakumwamba+ wandipatsa+ maufumu onse a padziko lapansi. Iye wandituma kuti ndim’mangire nyumba ku Yerusalemu+ m’dziko la Yuda. Danieli 5:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 “PERESI,* ufumu wanu wagawanika ndipo waperekedwa kwa Amedi ndi Aperisiya.”+
2 “Koresi mfumu ya Perisiya wanena kuti,+ ‘Yehova Mulungu wakumwamba+ wandipatsa+ maufumu onse a padziko lapansi. Iye wandituma kuti ndim’mangire nyumba ku Yerusalemu+ m’dziko la Yuda.