Mlaliki 10:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ngakhale m’chipinda chako, usanenere mfumu zoipa,+ ndipo m’zipinda zimene umagona usanenere zoipa aliyense wolemera,+ chifukwa cholengedwa chouluka chikanena mawu ako ndipo chinachake chokhala ndi mapiko chikaulula zimene wanena.+
20 Ngakhale m’chipinda chako, usanenere mfumu zoipa,+ ndipo m’zipinda zimene umagona usanenere zoipa aliyense wolemera,+ chifukwa cholengedwa chouluka chikanena mawu ako ndipo chinachake chokhala ndi mapiko chikaulula zimene wanena.+