Ekisodo 10:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pamenepo Yehova anauza Mose kuti: “Tambasula dzanja lako ndi kuloza kumwamba+ kuti m’dziko lonse la Iguputo mugwe mdima wandiweyani.” Yobu 33:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Kum’bweza kuti asapite kudzenje,+Kuti aunikiridwe ndi kuwala kwa anthu amene ali moyo.+
21 Pamenepo Yehova anauza Mose kuti: “Tambasula dzanja lako ndi kuloza kumwamba+ kuti m’dziko lonse la Iguputo mugwe mdima wandiweyani.”