Yobu 24:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Monga mbidzi+ m’chipululu,Osaukawo amapita kukafunafuna chakudya.Chipululu chimapatsa aliyense chakudya cha ana ake. Salimo 104:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Akasupewo amapereka madzi kwa zilombo zonse zakutchire.+Nthawi zonse mbidzi+ zimapha ludzu lawo mmenemo.
5 Monga mbidzi+ m’chipululu,Osaukawo amapita kukafunafuna chakudya.Chipululu chimapatsa aliyense chakudya cha ana ake.
11 Akasupewo amapereka madzi kwa zilombo zonse zakutchire.+Nthawi zonse mbidzi+ zimapha ludzu lawo mmenemo.