-
Zekariya 5:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Ndiyeno ndinakweza maso ndipo ndinaona akazi awiri akubwera. Akaziwo anali kuuluka ndi mapiko ooneka ngati a dokowe ndipo mphepo inali kuwomba mapikowo. Iwo ananyamula chiwiya choyezera chija n’kupita nacho m’mwamba, pakati pa dziko lapansi ndi kumwamba.
-