Yesaya 37:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Chifukwa kundipsera mtima kwako+ ndi kufuula kwako zafika m’makutu mwanga.+Ndithu ndidzakola mphuno yako ndi ngowe yanga, ndipo ndidzamanga zingwe zanga pakamwa pako.+Kenako ndidzakukoka n’kukubweza kudzera njira imene unadutsa pobwera.”+
29 Chifukwa kundipsera mtima kwako+ ndi kufuula kwako zafika m’makutu mwanga.+Ndithu ndidzakola mphuno yako ndi ngowe yanga, ndipo ndidzamanga zingwe zanga pakamwa pako.+Kenako ndidzakukoka n’kukubweza kudzera njira imene unadutsa pobwera.”+