Oweruza 20:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pakati pa anthu onsewa, panali anthu amanzere+ 700 osankhidwa mwapadera. Aliyense wa anthu amenewa anali wamaluli poponya miyala*+ ndipo sanali kuphonya. 2 Mbiri 26:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Uziya anapitiriza kukonzera gulu lankhondo lonselo zishango,+ mikondo ing’onoing’ono,+ zisoti,+ zovala za mamba achitsulo,+ mauta,+ ndi miyala yoponya ndi gulaye.*+
16 Pakati pa anthu onsewa, panali anthu amanzere+ 700 osankhidwa mwapadera. Aliyense wa anthu amenewa anali wamaluli poponya miyala*+ ndipo sanali kuphonya.
14 Uziya anapitiriza kukonzera gulu lankhondo lonselo zishango,+ mikondo ing’onoing’ono,+ zisoti,+ zovala za mamba achitsulo,+ mauta,+ ndi miyala yoponya ndi gulaye.*+