Yobu 11:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Bwenzi atakuuza chinsinsi cha nzeru,Chifukwa zinthu za nzeru ndiponso zopindulitsa n’zambiri.Komanso bwenzi utadziwa kuti Mulungu wachititsa kuti zolakwa zako zina ziiwalike.+ Yobu 15:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iyetu alibe chikhulupiririro mwa angelo* ake,+Ndipo kumwamba si koyera m’maso mwake.+ Yobu 22:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Kodi mwamuna wamphamvu angakhale waphindu kwa Mulungu?+Kodi aliyense wozindikira angakhale waphindu kwa iye?
6 Bwenzi atakuuza chinsinsi cha nzeru,Chifukwa zinthu za nzeru ndiponso zopindulitsa n’zambiri.Komanso bwenzi utadziwa kuti Mulungu wachititsa kuti zolakwa zako zina ziiwalike.+
2 “Kodi mwamuna wamphamvu angakhale waphindu kwa Mulungu?+Kodi aliyense wozindikira angakhale waphindu kwa iye?