Mateyu 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Mukamakhululukira anthu machimo awo, inunso Atate wanu wakumwamba adzakukhululukirani.+