Miyambo 24:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Usanene kuti: “Ndim’chitira zimene iye anandichitira.+ Aliyense ndizim’bwezera mogwirizana ndi zimene anachita.”+ Aroma 12:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Sangalalani ndi anthu amene akusangalala.+ Lirani ndi anthu amene akulira.
29 Usanene kuti: “Ndim’chitira zimene iye anandichitira.+ Aliyense ndizim’bwezera mogwirizana ndi zimene anachita.”+