Levitiko 19:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Uza khamu lonse la ana a Isiraeli kuti, ‘Mukhale oyera,+ chifukwa ine Yehova Mulungu wanu ndine woyera.+ Hoseya 11:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Sindidzasonyeza mkwiyo wanga woyaka moto.+ Sindidzawononganso Efuraimu+ pakuti ndine Mulungu+ osati munthu. Ndine Woyera pakati panu+ ndipo sindidzabwera kwa inu nditakwiya. 1 Petulo 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma khalani motsanzira Woyera amene anakuitanani. Inunso khalani oyera m’makhalidwe anu onse,+
2 “Uza khamu lonse la ana a Isiraeli kuti, ‘Mukhale oyera,+ chifukwa ine Yehova Mulungu wanu ndine woyera.+
9 Sindidzasonyeza mkwiyo wanga woyaka moto.+ Sindidzawononganso Efuraimu+ pakuti ndine Mulungu+ osati munthu. Ndine Woyera pakati panu+ ndipo sindidzabwera kwa inu nditakwiya.