Yobu 7:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kumbukirani kuti moyo wanga uli ngati mphepo,+Ndiponso kuti diso langa silidzaonanso zabwino. Salimo 103:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Masiku a moyo wa munthu ali ngati masiku a udzu wobiriwira.+Iye amaphuka ngati mmene duwa lakutchire limaphukira.+
15 Masiku a moyo wa munthu ali ngati masiku a udzu wobiriwira.+Iye amaphuka ngati mmene duwa lakutchire limaphukira.+