Yesaya 21:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mubweretse madzi podzakumana ndi munthu waludzu. Inu anthu okhala ku Tema,+ mukhale ndi chakudya podzakumana ndi munthu amene akuthawa. Yeremiya 25:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndinamwetsanso Dedani,+ Tema,+ Buza, onse odulira ndevu zawo zam’mbali,+
14 Mubweretse madzi podzakumana ndi munthu waludzu. Inu anthu okhala ku Tema,+ mukhale ndi chakudya podzakumana ndi munthu amene akuthawa.