Yobu 16:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kodi mawu opanda pakewa saatha?+Kapena chikukupwetekani n’chiyani kuti muziyankha? Yobu 21:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Choncho, amuna inu mukungodzivuta poyesa kunditonthoza,+Ndipo mayankho anu ndi mabodza okhaokha.”