Yobu 14:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Siyani kumuyang’anitsitsa kuti apumule,+Mpaka apeze chisangalalo ngati mmene amachitira waganyu pakutha pa tsiku. Salimo 39:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Inu Yehova, ndidziwitseni za kufulumira kwa chimaliziro changa,+Ndiponso kuti masiku anga ndi ochepa motani,+Kuti ndidziwe kufupika kwa moyo wanga.+
6 Siyani kumuyang’anitsitsa kuti apumule,+Mpaka apeze chisangalalo ngati mmene amachitira waganyu pakutha pa tsiku.
4 “Inu Yehova, ndidziwitseni za kufulumira kwa chimaliziro changa,+Ndiponso kuti masiku anga ndi ochepa motani,+Kuti ndidziwe kufupika kwa moyo wanga.+