Yesaya 25:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Monga momwe mthunzi wa mtambo umachepetsera kutentha m’dziko lopanda madzi, inu mumachepetsa phokoso la alendo.+ Nayonso nyimbo ya anthu ankhanza yaletsedwa.+
5 Monga momwe mthunzi wa mtambo umachepetsera kutentha m’dziko lopanda madzi, inu mumachepetsa phokoso la alendo.+ Nayonso nyimbo ya anthu ankhanza yaletsedwa.+