Yobu 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno Yobu anatenga phale loti azidzikanda nalo ndipo anali kukhala paphulusa.+ Yobu 30:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Usiku mafupa anga+ amabooledwa n’kugwa pansi.Zowawa zonditafuna sizipuma.+