Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 27:46
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 46 Zitatha izi, Rabeka anali kuuza Isaki nthawi ndi nthawi kuti: “Ndafika ponyansidwa nawo moyo wanga chifukwa cha ana aakazi achihetiwa.+ Ngati Yakobo atenga mkazi kuno pakati pa ana achiheti ngati amenewa, ndi bwino ndingofa!”+

  • 1 Mafumu 19:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 ndipo iyeyo analowa m’chipululu n’kuyenda ulendo wa tsiku limodzi. Kenako anafika pa kamtengo kenakake,+ ndipo anakhala pansi pake. Ndiyeno anayamba kupempha kuti afe, ponena kuti: “Basi ndatopa nazo. Tsopano chotsani moyo wanga+ Yehova, pakuti sindine woposa makolo anga.”

  • Yobu 10:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 “Ineyo ndikunyansidwa ndi moyo wanga.+

      Ndilankhula mwamphamvu za nkhawa zanga.

      Ndilankhula chifukwa cha kuwawa kwa moyo wanga.

  • Yona 4:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Tsopano inu Yehova, chotsani moyo wanga,+ pakuti kuli bwino kuti ndife kusiyana n’kukhala ndi moyo.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena