Salimo 62:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndithudi, ana a anthu ochokera kufumbi ali ngati mpweya,+Ana a anthu ndi malo othawirako achinyengo.+Onse pamodzi akaikidwa pasikelo ndi opepuka kuposa mpweya.+ Salimo 144:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Munthu amafanana ndi mpweya wotuluka m’mphuno.+Masiku ake ali ngati mthunzi wongodutsa.+ Mlaliki 6:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chifukwa chakuti pali zambiri zoyambitsa zinthu zachabe,+ kodi munthu amapindula chiyani?
9 Ndithudi, ana a anthu ochokera kufumbi ali ngati mpweya,+Ana a anthu ndi malo othawirako achinyengo.+Onse pamodzi akaikidwa pasikelo ndi opepuka kuposa mpweya.+