Salimo 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndimaganiza kuti: Munthu+ ndani kuti muzimuganizira,+Ndipo mwana wa munthu wochokera kufumbi ndani kuti muzimusamalira?+ Salimo 103:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Masiku a moyo wa munthu ali ngati masiku a udzu wobiriwira.+Iye amaphuka ngati mmene duwa lakutchire limaphukira.+ Salimo 144:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inu Yehova, munthu ndani kuti mumuganizire?+Kodi mwana wa munthu wochokera kufumbi+ ndani kuti mumuwerengere? Aheberi 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma mboni ina inachitira umboni penapake, kuti: “Munthu ndani kuti muzimuganizira,+ kapena mwana wa munthu ndani kuti muzimusamalira?+
4 Ndimaganiza kuti: Munthu+ ndani kuti muzimuganizira,+Ndipo mwana wa munthu wochokera kufumbi ndani kuti muzimusamalira?+
15 Masiku a moyo wa munthu ali ngati masiku a udzu wobiriwira.+Iye amaphuka ngati mmene duwa lakutchire limaphukira.+
3 Inu Yehova, munthu ndani kuti mumuganizire?+Kodi mwana wa munthu wochokera kufumbi+ ndani kuti mumuwerengere?
6 Koma mboni ina inachitira umboni penapake, kuti: “Munthu ndani kuti muzimuganizira,+ kapena mwana wa munthu ndani kuti muzimusamalira?+