Yesaya 59:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iwo aikira mazira a njoka yapoizoni, ndipo ankangokhalira kuluka ukonde wa kangaude.+ Aliyense wodya mazira a njoka yapoizoniyo amafa, ndipo dzira limene laswedwa limaswa mphiri.+
5 Iwo aikira mazira a njoka yapoizoni, ndipo ankangokhalira kuluka ukonde wa kangaude.+ Aliyense wodya mazira a njoka yapoizoniyo amafa, ndipo dzira limene laswedwa limaswa mphiri.+