Salimo 40:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Inu Yehova Mulungu wanga, mwatichitira zinthu zambiri zodabwitsa,+Ndipo mumatiganizira.+Palibe angafanane ndi inu.+Ndikafuna kulankhula ndi kunena za zodabwitsazo,Zimachuluka kwambiri moti sindingathe kuzifotokoza.+
5 Inu Yehova Mulungu wanga, mwatichitira zinthu zambiri zodabwitsa,+Ndipo mumatiganizira.+Palibe angafanane ndi inu.+Ndikafuna kulankhula ndi kunena za zodabwitsazo,Zimachuluka kwambiri moti sindingathe kuzifotokoza.+