Salimo 102:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Iye adzamvetsera pemphero la anthu amene alandidwa chilichonse,+Ndipo sadzapeputsa pemphero lawo.+ Miyambo 15:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Yehova amakhala kutali ndi anthu oipa,+ koma amamva pemphero la anthu olungama.+
17 Iye adzamvetsera pemphero la anthu amene alandidwa chilichonse,+Ndipo sadzapeputsa pemphero lawo.+