Salimo 73:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndithudi, ndayeretsa mtima wanga pachabe,+Ndipo ndasamba m’manja mwanga pachabe posonyeza kuti ndine wopanda cholakwa.+ Yeremiya 2:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 “Koma iwe ukuti, ‘Ine ndilibe mlandu uliwonse. Ndithudi mkwiyo wake wandichokera.’+ “Tsopano ndikuyamba kukuimba mlandu chifukwa chonena kuti, ‘Sindinachimwe.’+
13 Ndithudi, ndayeretsa mtima wanga pachabe,+Ndipo ndasamba m’manja mwanga pachabe posonyeza kuti ndine wopanda cholakwa.+
35 “Koma iwe ukuti, ‘Ine ndilibe mlandu uliwonse. Ndithudi mkwiyo wake wandichokera.’+ “Tsopano ndikuyamba kukuimba mlandu chifukwa chonena kuti, ‘Sindinachimwe.’+