Salimo 139:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mafupa anga sanali obisika kwa inu+Pamene munali kundipanga m’malo obisika,+Pamene munali kundiwomba ngati nsalu m’malo apansi kwambiri+ padziko lapansi.
15 Mafupa anga sanali obisika kwa inu+Pamene munali kundipanga m’malo obisika,+Pamene munali kundiwomba ngati nsalu m’malo apansi kwambiri+ padziko lapansi.