Yobu 9:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ngati ndanena kuti, ‘Ndiiwale nkhawa zanga,+Ndisinthe maonekedwe anga+ ndi kusangalala,’ Salimo 39:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Musandiyang’ane mutakwiya, kuti ndikhalenso wosangalala+Ndisanamwalire ndi kuiwalika.”+